Ngati 5% ya anthu okwana 18 million amene ali mziko muno itatukuka muchuma kudzera mu ma share pofika zaka 5 kuchokera pano Malawi sangakhale chimodzimodzi
2024-03-01 11:54:26
Tenganipo mbali pokweza chuma Cha dziko la Malawi pakuthandizira kuphelezera masophenya a dziko a 2063 pakukhala ndi ma shares mma kampani amene Ali pa mndandanda wa Malawi Stock Exchange.
2024-03-01 13:48:33
We are talking of the practical and real economic life experience that positively transforms peoples lives. "Shareholding.
2024-03-01 13:55:28
MISALICO will be extending it's shareholding literacy program to the central region under the theme "creating and building wealth through the Malawi Stock Exchange"
2024-03-01 14:10:03
Questions were asked and were answered. We had the opportunity to know and interact with Fund Managers, Transfer Secretaries and the Blockers.
18:00